2 Chronicles 20:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kenaka Alevi, ana a Kohati ndi ana a Kora, adaimirira kuti atamande Chauta, Mulungu wa Aisraele, mokweza kwambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Alevi, a ana a Akohati, ndi a ana a Kora, anauka kulemekeza Yehova Mulungu wa Israele ndi mau omveketsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka Alevi ena ochokera ku mabanja a Kohati ndi Kora anayimirira ndipo anatamanda Yehova Mulungu wa Israeli ndi mawu ofuwula kwambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Alevi, a ana a Akohati, ndi a ana a Kora, anauka kulemekeza Yehova Mulungu wa Israyeli ndi mau omveketsa.