2 Chronicles 20:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa tsiku lachinai lake, adasonkhana ku chigwa cha Beraka, ndipo kumeneko adatamanda Chauta. Nchifukwa chake malowo amatchedwa chigwa cha Beraka mpaka lero lino.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi tsiku lachinai anasonkhana m'chigwa cha Beraka; pakuti pamenepo analemekeza Yehova; chifukwa chake anatcha dzina lake la malowo, Chigwa cha Beraka, mpaka lero lino.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsiku lachinayi anasonkhana ku chigwa cha Beraka kumene anatamanda Yehova. Nʼchifukwa chake malowa amatchedwa chigwa cha Beraka mpaka lero.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi tsiku lacinai anasonkhana m'cigwa ca Beraka; pakuti pamenepo analemekeza Yehova; cifukwa cace anacha dzina lace la malowo, Cigwa ca Beraka, mpaka lero lino.