2 Chronicles 20:29 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo maufumu onse a m'maiko achilendowo adachita mantha kwambiri, atamva kuti Chauta ndiye adathira nkhondo pa adani a Aisraele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kuopsa kwa Mulungu kunagwera maufumu onse a m'maiko, pamene anamva kuti Yehova adayambana ndi adani a Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kuopsa kwa Mulungu kunali pa maufumu onse a mayiko amene anamva mmene Yehova anamenyera adani a Aisraeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kuopsa kwa Mulungu kunagwera maufumu onse a m'maiko, pamene anamva kuti Yehova adayambana ndi adani a Israyeli.