2 Chronicles 20:35 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zitapita zimenezi, Yehosafati mfumu ya ku Yuda, adagwirizana ndi Ahaziya mfumu ya ku Israele, amene ankachita zoipa kwambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Zitatha izi, Yehosafati mfumu ya Yuda anaphatikana ndi Ahaziya mfumu ya Israele, yemweyo anachita moipitsitsa;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zitapita izi, Yehosafati mfumu ya Yuda inachita mgwirizano ndi Ahaziya mfumu ya Israeli, amene anachita zoyipa kwambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Zitathaizi, Yehosafati mfumu ya Yuda anaphatikana ndi Ahaziya mfumu ya Israyeli, yemweyo anacita moipitsitsa;