2 Chronicles 20:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ayuda onse adasonkhana kuti adzapemphe chithandizo kwa Chauta. Anthu onse a ku mizinda yonse ya ku Yuda adabwera kudzapempha chithandizo kwa Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Namemezedwa Yuda afunsire kwa Yehova, inde anachokera kumidzi yonse ya Yuda kufuna Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu a ku Yuda anabwera pamodzi kudzafuna thandizo kwa Yehova, ndipo anabweradi kuchokera ku mzinda uliwonse wa mu Yuda kudzafunafuna Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Namemezedwa Yuda afunsire kwa Yehova, inde anacokera ku midzi yonse ya Yuda kufuna Yehova.