2 Chronicles 20:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Yehosafati adaimirira pakati pa msonkhano wa Ayuda ku Yerusalemu m'Nyumba ya Chauta pa bwalo latsopano.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yehosafati anaima mu msonkhano wa Ayuda, ndi a ku Yerusalemu, kunyumba ya Yehova, pakati pa bwalo latsopano;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehosafati anayimirira pakati pa msonkhano wa Yuda ndi Yerusalemu, pa Nyumba ya Yehova patsogolo pa bwalo latsopano
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yehosafati anaima mu msonkhano wa Ayuda, ndi a ku Yerusalemu, ku nyumba ya Yehova, pakati pa bwalo latsopano;