2 Chronicles 20:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwakuti iwo atakhazikika m'dziko limenelo, adakumangirani Nyumba m'menemo, nkumati,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nakhala m'mwemo iwowa, nakumangirani m'mwemo malo opatulika a dzina lanu, ndi kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo akhala mʼdzikolo ndipo anamangira Dzina lanu malo opatulika, nʼkumati,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nakhala m'mwemo iwowa, nakumangirani m'mwemo malo opatulika a dzina lanu, ndi kuti,