2 Chronicles 21:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chifukwa cha zonsezi Chauta adzaŵagwetsera mliri anthu ako, ana ako, akazi ako, ndi zinthu zako zonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
taonani, Yehova adzakantha anthu anu, ndi ana anu, ndi akazi anu, ndi chuma chanu chonse, makanthidwe akulu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kotero tsono Yehova ali pafupi kukantha anthu ako, ana ako, akazi ako ndi zinthu zako zonse, ndi chilango chachikulu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
taonani, Yehova adzakantha anthu anu, ndi ana anu, ndi akazi anu, ndi cuma canu conse, makanthidwe akuru;