2 Chronicles 21:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo iweyo udzadwala nthenda yoopsa ya m'mimba imene izidzakulirakulira tsiku ndi tsiku mpaka matumbo ako adzasololoka.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo mudzadwala kwakukulu nthenda yamatumbo, mpaka matumbo anu adzatuluka chifukwa cha nthendayi tsiku ndi tsiku.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo iwe udzadwala nthenda yoopsa yamʼmimba, mpaka nthendayo idzachititsa matumbo ako kutuluka.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo mudzadwala kwakukuru nthenda yamatumbo, mpaka matumbo anu adzaturuka cifukwa ca nthendayi tsiku ndi tsiku.