2 Chronicles 21:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Abale ake, ana a Yehosafati, anali aŵa: Azariya, Yehiyele, Zekariya, Azariyahu, Mikaele ndi Sefatiya. Onseŵa anali ana a Yehosafati, mfumu ya ku Yuda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anali nao abale ake, ana a Yehosafati, Azariya, ndi Yehiyele, ndi Zekariya, ndi Azariya, ndi Mikaele, ndi Sefatiya, onsewa ndiwo ana a Yehosafati mfumu ya Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Abale ake a Yehoramu, ana aamuna a Yehosafati, anali Azariya, Yehieli, Zekariya, Azariyahu, Mikayeli ndi Sefatiya. Onsewa anali ana a Yehosafati mfumu ya Israeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anali nao abale ace, ana a Yehosafati, Azariya, ndi Yehieli, ndi Zekariya, ndi Azariya, ndi Mikaeli, ndi Sefatiya, onsewa ndiwe ana a Yehosafati mfumu ya Israyeli.