2 Chronicles 21:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yehoramu anali wa zaka 32 pamene adaloŵa ufumu, ndipo adalamulira zaka zisanu ndi zitatu ku Yerusalemu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehoramu anali wa zaka makumi atatu mphambu ziwiri polowa ufumu wake, nachita ufumu m'Yerusalemu zaka zisanu ndi zitatu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehoramu anali wa zaka 32 pamene anakhala mfumu, ndipo analamulira mu Yerusalemu zaka zisanu ndi zitatu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehoramu anali wa zaka makumi atatu mphambu ziwiri polowa ufumu wace, nacita ufumu m'Yerusalemu zaka zisanu ndi zitatu.