2 Chronicles 21:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe Chauta sadafune kuononga banja la Davide, chifukwa cha chipangano chimene adaachita ndi Davide, ndiponso poti adaalonjeza kuti adzampatsa nyale Davide ndi zidzukulu zake mpaka muyaya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Yehova sanafune kuononga nyumba ya Davide chifukwa cha pangano adalichita ndi Davide, ndi monga adalonjeza kumpatsa iye ndi ana ake nyali nthawi zonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komabe, chifukwa cha pangano limene Yehova anachita ndi Davide, Yehova sanafune kuwononga banja la Davide. Iye analonjeza kusungira nyale Davide ndi zidzukulu zake mpaka muyaya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Yehova sanafuna kuononga nyumba ya Davide cifukwa ca pangano adalicita ndi Davide, ndi monga adalonjeza kumpatsa iye ndi ana ace nyali nthawi zonse.