2 Chronicles 23:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero anthu onse am'dzikomo adakondwa. Ndipo mumzindamo mudakhala bata, Ataliya ataphedwa ndi lupanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anthu onse a m'dziko anakondwera; ndi m'mudzi munali chete, atamupha Ataliya ndi lupanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo anthu onse a mʼderali anakondwera. Tsono mu mzinda munali bata chifukwa Ataliya anaphedwa ndi lupanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anthu onse a m'dziko anakondwera; ndi m'mudzi munali cete, atamupha Ataliya ndi lupanga.