2 Chronicles 23:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Gulu lachiŵiri lidzalonde ku nyumba ya mfumu, gulu lachitatu lidzalonde pa khomo lakuchipata. Ndipo anthu onse adzakhale m'mabwalo a Nyumba ya Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi limodzi la magawo atatu likhale kunyumba ya mfumu; ndi limodzi la magawo atatu ku Chipata cha Maziko; ndi anthu onse akhale m'mabwalo a nyumba ya Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndi limodzi la magawo atatu likakhale ku nyumba yaufumu ndipo limodzi la magawo atatu likakhale ku chipata cha Maziko ndipo anthu ena onse akakhale mʼmabwalo a Nyumba ya Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi limodzi la magawo atatu likhale ku nyumba ya mfumu; ndi limodzi la magawo atatu ku cipata ca maziko; ndi anthu onse akhale m'mabwalo a nyumba ya Yehova.