2 Chronicles 24:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yowasi anali wa zaka zisanu ndi ziŵiri pamene adaloŵa ufumu, ndipo adalamulira zaka 40 ku Yerusalemu. Mai wake anali Zibiya wa ku Beereseba.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yowasi anali wa zaka zisanu ndi ziwiri polowa ufumu wake, nakhala mfumu m'Yerusalemu zaka makumi anai; ndi dzina la make ndiye Zibiya wa ku Beereseba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yowasi anali wa zaka zisanu ndi ziwiri pamene anakhala mfumu, ndipo analamulira mu Yerusalemu kwa zaka makumi anayi. Dzina la amayi ake linali Zibiya wa ku Beeriseba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yoasi anali wa zaka zisanu ndi ziwiri polowa ufumu wace, nakhala mfumu m'Yerusalemu zaka makumi anai; ndi dzina la mace ndiye Zibiya wa ku Beereseba.