2 Chronicles 24:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Yehoyada adakalamba kwambiri, masiku ake adachuluka, ndipo adamwalira ali wa zaka 130.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Yehoyada anakalamba, nachuluka masiku, namwalira iye; ndiye wa zaka zana limodzi mphambu makumi atatu pamene anamwalira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono Yehoyada anakalamba ndipo anali ndi zaka zambiri. Pambuyo pake iye anamwalira ali ndi zaka 130.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Yehoyada anakalamba, nacuruka masiku, namwalira iye; ndiye wa zaka zana limodzi mphambu makumi atatu pamene anamwalira.