2 Chronicles 24:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adamuika m'manda ku mzinda wa Davide pamodzi ndi mafumu, chifukwa chakuti adaachita zabwino m'dziko la Israele ndipo ankatumikira Mulungu ndi Nyumba yake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anamuika m'mudzi wa Davide, pakati pa mafumu; pakuti anachita zabwino m'Israele, ndi kwa Mulungu, ndi kunyumba yake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iyeyo anayikidwa mʼmanda pamodzi ndi mafumu mu mzinda wa Davide chifukwa cha zabwino zimene anachita mu Israeli, kuchitira Mulungu ndi Nyumba yake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anamuika m'mudzi wa Davide, pakati pa mafumu; pakuti anacita zabwino m'Israyeli, ndi kwa Mulungu, ndi ku nyumba yace.