2 Chronicles 24:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero mfumu Yowasi sadakumbukire zabwino zimene Yehoyada bambo wake wa Zekariya adamchitira, koma adapha mwana wake. Ndipo pamene ankafa, mwanayo adati, “Chauta apenye, ndipo abwezere chilango.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Motero mfumu Yowasi sanakumbukire zokoma anamchitirazi Yehoyada atate wake, koma anapha mwana wake; ndiye pomwalira anati, Yehova achipenye, nachifunse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mfumu Yowasi sinakumbukire zabwino zimene Yehoyada abambo ake a Zekariya anamuchitira, koma anapha mwana wake. Pamene amafa, iye ananena kuti, “Yehova aone zimenezi ndipo abwezere chilango.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Motero mfumu Yoasi sanakumbukila zokoma anamcitirazi Yehoyada atate wace, koma anapha mwana wace; ndiye pomwalira anati, Yehova acipenye, nacifunse.