2 Chronicles 24:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu amene adamchita chiwembuwo ndi Zabadi mwana wa Simea Mwamoni, ndi Yehozabadi mwana wa Simeriti Mmowabu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Omchitira chiwembu ndi awa: Zabadi, mwana wa Simeati wamkazi Mwamoni; ndi Yehozabadi, mwana wa Simiriti wamkazi Mmowabu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo amene anamuchitira chiwembu anali Zabadi mwana wa Simeati, mkazi wa ku Amoni, ndi Yehozabadi mwana wa Simiriti, mkazi wa ku Mowabu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Omcitira ciwembu ndi awa: Zabadi, mwana wa Simeati wamkazi M-amoni; ndi Yozabadi, mwana wa Simiriti wamkazi Mmoabu.