2 Chronicles 24:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yehoyada adaipezera mfumuyo akazi aŵiri, ndipo idabereka ana aamuna ndi ana aakazi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yehoyada anamtengera akazi awiri, nabala ana aamuna ndi aakazi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehoyada anamupezera iye akazi awiri, ndipo anabereka ana aamuna ndi aakazi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yehoyada anamtengera akazi awiri, nabala ana amuna ndi akazi.