2 Chronicles 24:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo adalengeza kwa anthu onse a ku Yuda ndi a mu Yerusalemu, kuti adzapereke kwa Chauta ndalama zimene Mose mtumiki wa Mulungu adaalamula kuchipululu kuja kuti Aisraele onse azipereka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nalalikira mwa Yuda ndi Yerusalemu, abwere nao kwa Yehova msonkho umene Mose mtumiki wa Mulungu anauikira Aisraele m'chipululu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo analengeza kwa anthu a mu Yuda ndi mu Yerusalemu kuti abweretse kwa Yehova msonkho umene Mose mtumiki wa Mulungu analamulira Aisraeli mʼchipululu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nalalikira mwa Yuda ndi Yerusalemu, abwere nao kwa Yehova msonkho umene Mose mtumiki wa Mulungu anauikira Aisrayeli m'cipululu.