2 Chronicles 25:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adamnyamulira pa kavalo, nadzamuika m'manda momwe adaikidwa makolo ake mu mzinda wa Davide.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Namnyamula pa akavalo, namuika pamodzi ndi makolo ake m'mudzi wa Yuda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anabwera naye ali pa kavalo ndipo anayikidwa mʼmanda ndi makolo ake mu mzinda wa Yuda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Namnyamula pa akavalo, namuika pamodzi ndi makolo ace m'mudzi wa Yuda.