2 Chronicles 25:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono atangolandira mphamvu zonse zaufumu m'manja mwake, adapha anyamata ake amene adaapha mfumu ija, bambo wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kunachitika tsono, utamkhazikikira ufumu, anapha anyamata ake amene adapha mfumu atate wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene mphamvu zonse zaufumu zinali mʼmanja mwake, iye anapha akuluakulu amene anapha abambo ake, mfumu ija.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kunacitika tsono, utamkhazikikira ufumu, anapha anyamata ace amene adapha mfumu atate wace.

Recommended Reading