2 Chronicles 25:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adalembanso anthu ankhondo amphamvu ndi olimba mtima a ku Israele, okwanira 100,000, pa mtengo wa makilogramu 3,400 a siliva.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Analemberanso ngwazi zamphamvu za m'Israele zikwi zana limodzi, kuwalipira matalente a siliva zana limodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye analembanso ntchito anthu odziwa nkhondo 100,000 ochokera ku Israeli pa mtengo wa makilogalamu 3,400 a siliva.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Analemberanso ngwazi zamphamvu za m'Israyeli zikwi zana limodzi, kuwalipira matalente a siliva zana limodzi.