2 Chronicles 26:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake anthu onse a ku Yuda adatenga Uziya, wa zaka 16, namlonga ufumu m'malo mwa Amaziya bambo wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anthu onse Ayuda anatenga Uziya, ndiye wa zaka khumi mphambu zisanu ndi chimodzi, namlonga ufumu m'malo mwa atate wake Amaziya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka anthu onse a ku Yuda anatenga Uziya amene anali wa zaka 16, namuyika kukhala mfumu mʼmalo mwa Amaziya abambo ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anthu onse Ayuda anatenga Uziya, ndiye wa zaka khumi mphambu zisanu ndi cimodzi, namlonga ufumu m'malo mwa atate wace Amaziya.