2 Chronicles 27:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iyeyo adamanga khomo lapamwamba la ku Nyumba ya Chauta, ndipo adagwira ntchito yaikulu yomanga linga la Ofele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anamanga chipata cha kumtunda cha nyumba ya Yehova, ndi pa linga la Ofele anamanga kwakukulu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yotamu anamanganso chipata chakumtunda cha Nyumba ya Yehova ndipo anagwira ntchito yayikulu yomanga khoma la ku phiri la Ofeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anamanga cipata ca kumtunda ca nyumba ya Yehova, ndi pa linga la Ofeli anamanga kwakukuru.