2 Chronicles 27:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komanso adamanga mizinda ku dziko lonse lamapiri la Yuda. Adamanganso malinga ndi nsanja ku nkhalango zakumapiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Namanga midzi m'mapiri a Yuda, ndi m'nkhalango anamanga nyumba zansanja, ndi nsanja zomwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anamanga mizinda mʼmapiri a ku Yuda ndipo anamanganso malinga ndi nsanja mʼmadera a ku nkhalango.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Namanga midzi m'mapiri a Yuda, ndi m'nkhalango anamanga nyumba zansanja, ndi nsanja zomwe.