2 Chronicles 27:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iyeyo anali wa zaka 25 pamene ankaloŵa ufumu, ndipo adalamulira zaka 16 ku Yerusalemu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anali wa zaka makumi awiri mphambu zisanu polowa ufumu wake, nakhala mfumu m'Yerusalemu zaka khumi mphambu zisanu ndi chimodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anakhala mfumu ali ndi zaka 25 ndipo analamulira mu Yerusalemu kwa zaka 16.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anali wa zaka makumi awiri mphambu zisanu polowa ufumu wace, nakhala mfumu m'Yerusalemu zaka khumi mphambu zisanu ndi cimodzi.