2 Chronicles 27:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake Yotamu adamwalira, naikidwa m'manda mu mzinda wa Davide. Ndipo Ahazi mwana wake adaloŵa ufumu m'malo mwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yotamu anagona ndi makolo ake, namuika m'mudzi wa Davide; ndi Ahazi mwana wake anakhala mfumu m'malo mwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yotamu anamwalira ndipo anayikidwa mʼmanda mu Mzinda wa Davide. Ndipo Ahazi mwana wake analowa ufumu mʼmalo mwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yotamu anagona ndi makolo ace, namuika m'mudzi wa Davide; ndi Ahazi mwana wace anakhala mfumu m'malo mwace.