2 Chronicles 28:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adamanga akachisi opembedzerako ku mzinda uliwonse wa Yuda, kuti azifukizako lubani kwa milungu ina, kuputa mkwiyo wa Chauta, Mulungu wa makolo ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi m'midzi iliyonse ya Yuda anamanga misanje ya kufukizira milungu ina, nautsa mkwiyo wa Yehova Mulungu wa makolo ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mu mzinda uliwonse wa Yuda anamangamo malo achipembedzo, operekerapo nsembe zopsereza kwa milungu ina ndipo anaputa mkwiyo wa Yehova, Mulungu wa makolo ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi m'midzi iri yonse ya Yuda anamanga misanje ya kufukizira milungu yina, nautsa mkwiyo wa Yehova Mulungu wa makolo ace.