2 Chronicles 29:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono ine ndikuganiza kuti ndichite chipangano ndi Chauta, Mulungu wa Israele, kuti mkwiyo wake woopsawo utichoke.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsono mumtima mwanga nditi ndichite chipangano ndi Yehova Mulungu wa Israele, kuti mkwiyo wake waukali utembenuke kutichokera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono ine ndikuganiza zochita pangano ndi Yehova Mulungu wa Israeli, kuti mkwiyo wake woopsawu utichokere.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsono mumtima mwanga nditi ndicite cipangano ndi Yehova Mulungu wa Israyeli, kuti mkwiyo wace waukali utembenuke kuticokera.