2 Chronicles 29:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana anga, musachedwe, pakuti Chauta wakusankhani inu kuti muziima pamaso pake ndi kumamtumikira, ndipo kuti mukhale atumiki ake, ndi kumafukiza lubani kwa Iye.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ana anga, musazengereza tsopano; popeza Yehova anakusankhani inu muime pamaso pake, kumtumikira Iye, ndi kuti mukhale atumiki ake ndi kufukiza zonunkhira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana anga, musanyalanyaze tsopano, pakuti Yehova wakusankhani kuti muziyima pamaso pake ndi kumutumikira Iye, kugwira ntchito pamaso pake ndi kufukiza lubani.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ana anga, musazengereza tsopano; popeza Yehova anakusankhani inu muime pamaso pace, kumtumikira Iye, ndi kuti mukhale atumiki ace ndi kufukiza zonunkhira.