2 Chronicles 29:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Alevi amene anali pomwepo ndi aŵa: a m'banja la Kohati: Mahati mwana wa Amasai, ndi Yowele mwana wa Azariya; a m'banja la Merari: Kisi mwana wa Abidi, ndi Azariya mwana wa Yehalelele; a m'banja la Geresoni: Yowa mwana wa Zima, ndi Edeni mwana wa Yowa;
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo ananyamuka Alevi, Mahati mwana wa Amasai ndi Yowele mwana wa Azariya, a ana a Akohati; ndi a ana a Merari, Kisi mwana wa Abidi, ndi Azariya mwana wa Yehalelele; ndi a Ageresoni, Yowa mwana wa Zima, ndi Edeni mwana wa Yowa;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Alevi awa anakonzeka kugwira ntchito: Kuchokera ku banja la Kohati, Mahati mwana wa Amasai ndi Yoweli mwana wa Azariya; kuchokera ku banja la Merari, Kisi mwana wa Abidi ndi Azariya mwana wa Yehaleleli; kuchokera ku banja la Geresoni, Yowa mwana wa Zima ndi Edeni mwana wa Yowa;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo ananyamuka Alevi, Mahati mwana wa Amasai ndi Yoeli mwana wa Azariya, a ana a Akohati; ndi a ana a Merari, Kisi mwana wa Abidi, ndi Azariya mwana wa Yehaleleli; ndi a Agerisoni, Yowa mwana wa Zima, ndi Edeni mwana wa Yowa;