2 Chronicles 29:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zipangizo zonse zimene mfumu Ahazi adaazichotsa pamene anali mfumu yosakhulupirika, tazibwezera, ndipo taziyeretsa. Taziika ku guwa la Chauta.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Zipangizo zonse zomwe adazitaya mfumu Ahazi m'ufumu wake m'kulakwa kwake kuja, tazikonza, ndi kuzipatula; ndipo taonani, zili kuguwa la nsembe la Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Takonza ndi kuyeretsa zinthu zonse zimene mfumu Ahazi anazichotsa mwa kusakhulupirika kwake pamene anali mfumu. Taziyika kutsogolo kwa guwa la Yehova.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Zipangizo zonse zomwe adazitaya mfumu Ahazi m'ufumu wace m'kulakwa kwace kuja, tazikonza, ndi kuzipatula; ndipo taonani, ziri ku guwa la nsembe la Yehova.