2 Chronicles 29:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake mfumu Hezekiya adanyamuka m'mamaŵa, nasonkhanitsa akuluakulu amumzindamo, ndipo adakwera ku Nyumba ya Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo mfumu Hezekiya analawira mamawa, nasonkhanitsa akalonga a m'mudzi, nakwera kunka kunyumba ya Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mmamawa tsiku linalo, mfumu Hezekiya inasonkhanitsa pamodzi akuluakulu a mu mzindawo ndipo inapita ku Nyumba ya Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo mfumu Hezekiya analawira mamawa, nasonkhanitsa akalonga a m'mudzi, nakwera kumka ku nyumba ya Yehova.