2 Chronicles 29:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono atonde operekera nsembe yopepesera uchimo aja, adabwera nawo kwa mfumu ndi kwa msonkhano wonse. Ndipo adasanjika manja ao pa atondewo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo anayandikiza nao atonde a nsembe yauchimo pamaso pa mfumu ndi msonkhano; ndipo iwo anawasanjika manja ao,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mbuzi zoperekedwa chifukwa cha tchimo zija zinabweretsedwa pamaso pa mfumu ndi anthu onse, ndipo anasanjika manja awo pa izo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo anayandikiza nao atonde a nsembe yaucimo pamaso pa mfumu ndi msonkhano; ndipo iwo anawasanjika manja ao,