2 Chronicles 29:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo Hezekiya adalamula kuti nsembe yopsereza iperekedwe pa guwa. Atayamba kupereka nsembe yopsereza, adayambanso kuimbira nyimbo Chauta. Ndipo adaliza malipenga ndi zipangizo zoimbira za Davide mfumu ya Israele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nanena Hezekiya kuti apereke nsembe yopsereza pa guwa la nsembe. Ndipo pakuyamba nsembe yopsereza, inayambanso nyimbo ya Yehova ndi malipenga, pamodzi ndi zoimbira za Davideyo mfumu ya Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Hezekiya analamulira kuti apereke nsembe zopsereza pa guwa. Pamene amayamba kupereka nsembezo, kuyimbira Yehova kunayambikanso, pamodzi ndi malipenga ndi zipangizo zoyimbira za Davide mfumu ya Israeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nanena Hezekiya kuti apereke nsembe yopsereza pa guwa la nsembe. Ndipo pakuyamba nsembe yopsereza, inayambanso nyimbo ya Yehova ndi malipenga, pamodzi ndi zoyimbira za Davideyo mfumu ya Israyeli.