2 Chronicles 29:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Msonkhano wonse udagwada moŵeramitsa mitu pansi, anthu oimba nyimbo akuimba, ndipo oliza malipenga akuliza. Adakhala akuchita zimenezi mpaka nsembe yopsereza idatha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi msonkhano wonse unalambira, ndi amalipenga anaomba; zonsezi mpaka adatsiriza nsembe yopsereza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu onse anawerama pansi ndi kulambira, pamene oyimba amayimba ndi malipenga. Izi zonse zinapitirira mpaka pa mapeto pa nsembe zopsereza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi msonkhano wonse unalambira, ndi oyimbira anayimba, ndi amalipenga anaomba; zonsezi mpaka adatsiriza nsembe yopsereza.