2 Chronicles 29:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa chaka choyamba cha ufumu wake, pa mwezi woyamba, Hezekiya adatsekula zitseko za Nyumba ya Chauta, nazikonza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chaka choyamba cha ufumu wake, mwezi woyamba, anatsegula pa makomo a nyumba ya Yehova, napakonzanso.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa chaka choyamba cha ulamuliro wake, iye anatsekula zitseko za Nyumba ya Yehova ndipo anazikonza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Caka coyamba ca ufumu wace, mwezi woyamba, anatsegula pa makomo a nyumba ya Yehova, napakonzanso.