2 Chronicles 29:36 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho Hezekiya ndi anthu onse aja adakondwa chifukwa cha zimene Mulungu adaŵachitira, pakuti zimenezo zidaachitika mwadzidzidzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nakondwera Hezekiya ndi anthu onse pa ichi Mulungu adakonzeratu; pakuti chinthuchi chidachitika modzidzimutsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Hezekiya ndi anthu onse anakondwera pa zimene Mulungu anachitira anthu ake, chifukwa zinachita mwamsangamsanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nakondwera Hezekiya ndi anthu onse pa ici Mulungu adakonzeratu; pakuti cinthuci cidacitika modzidzimutsa.