2 Chronicles 29:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Makolo athu adaphedwa ndi lupanga, ndipo ana athu aamuna, ana athu aakazi ndi akazi athu ali ku ukapolo chifukwa cha zimenezi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti taonani, makolo athu adagwa ndi lupanga, ndi ana athu aamuna ndi aakazi ndi akazi athu ali andende chifukwa cha ichi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ichi nʼchifukwa chake makolo athu anaperekedwa ku lupanga ndipo nʼchifukwa chake ana athu aamuna ndi aakazi ndi akazi athu ali ku ukapolo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti taonani, makolo athu adagwa ndi lupanga, ndi ana athu amuna ndi akazi ndi akazi athu ali andende cifukwa ca ici.