2 Chronicles 3:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo Kerubi ameneyu phiko lake limodzi, la mamita aŵiri nkanthu, linkakhudza ku khoma la nyumba, phiko lake lina, nalonso la mamita aŵiri nkanthu, lidalumikizana ndi phiko la kerubi woyamba uja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi phiko la kerubi wina mikono isanu lojima khoma la nyumba, ndi phiko linzake mikono isanu lolumikizana ndi phiko la kerubi wina.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chimodzimodzinso phiko la Kerubi wachiwiri linali loposerapo mamita awiri ndipo limakhudza mbali ina ya khoma la Nyumba ya Mulungu, ndipo linalo limene linalinso loposera mamita awiri, limakhudza phiko la Kerubi woyamba uja.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi phiko la kerubi wina mikono isanu lojima khoma la nyumba, ndi phiko linzace mikono isanu lolumikizana ndi phiko la kerubi wina.