2 Chronicles 3:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mapiko a akerubi amenewo onse pamodzi akaŵatambasula ankakwanira mamita asanu ndi anai. Akerubiwo adaaimirira pa mapazi ao, kuyang'ana m'kati mwa nyumbayo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mapiko a akerubi awa anafunyululika mikono makumi awiri; ndipo anaima ndi mapazi ao, ndi nkhope zao zinaloza kukhomo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mapiko a Akerubiwa akawatambasula amatalika mamita asanu ndi anayi. Akerubiwa anayimirira pa mapazi awo, kuyangʼana chipinda chachikulu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mapiko a akerubi awa anafunyululika mikono makumi awiri; ndipo anaima ndi mapazi ao, ndi, nkhope zao zinaloza kukhomo.
Recommended Reading