2 Chronicles 30:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Dzanja la Mulungu linalinso ndi anthu a ku Yuda, kuti aŵapatse mtima umodzi wochita zimene mfumu ndi nduna zake adaalamula, monga momwe Chauta adaanenera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ku Yuda komwe kunali dzanja la Mulungu lakuwapatsa mtima umodzi, kuchita chowauza mfumu ndi akulu mwa mau a Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Dzanja la Mulungu linalinso pa anthu a ku Yuda, kuwapatsa mtima umodzi wochita zimene mfumu ndi akuluakulu ake analamula potsata mawu a Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ku Yuda komwe kunali dzanja la Mulungu lakuwapatsa mtima umodzi, kucita cowauza mfumu ndi akuru mwa mau a Yehova.