2 Chronicles 30:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndiye kuti chinamtindi cha anthu, ambiri mwa iwo a ku Efuremu, a ku Manase, a ku Isakara ndi a ku Zebuloni, anali oipitsidwa pa zachipembedzo. Koma adadya naobe Paska, monyozera mwambo wolamulidwa. Koma Hezekiya adaaŵapempherera kuti, “Chauta, Mulungu wabwino, mukhululukire munthu aliyense
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti, anthu aunyinji, ndiwo ambiri a Efuremu, ndi Manase, Isakara, ndi Zebuloni, sanadziyeretse, koma anadya Paska mosati monga munalembedwa. Koma Hezekiya anawapempherera, ndi kuti, Yehova wabwino akhululukire yense
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngakhale kuti ambiri mwa anthu ochokera ku Efereimu, Manase, Isakara ndi Zebuloni sanadziyeretse okha, komabe anadya Paska motsutsana ndi zimene zinalembedwa. Koma Hezekiya anawapempherera, kunena kuti, “Yehova wabwino, khululukirani aliyense
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti, anthu aunyinji, ndiwo ambiri a Efraimu, ndi Manase, Isakara, ndi Zebuloni, sanadziyeretsa, koma anadya Paskha mosati monga munalembedwa.