2 Chronicles 30:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakuti mfumu, nduna zake ndi anthu onse a ku Yerusalemu anali atapangana kuti azichita Paska pa mwezi wachiŵiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti mfumu idapangana ndi akulu ake, ndi msonkhano wonse wa m'Yerusalemu, kuti achite Paska mwezi wachiwiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mfumu ndi akuluakulu ake pamodzi ndi anthu onse a mu Yerusalemu anagwirizana kuti akondwerere Paska pa mwezi wachiwiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti mfumu idapangana ndi akuru ace, ndi msonkhano wonse wa m'Yerusalemu, kuti acite Paskha mwezi waciwiri.