2 Chronicles 30:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake msonkhano wonse udavomerezana zopitiriza chikondwererocho masiku asanu ndi aŵiri ena. Choncho adachitadi chikondwerero masiku asanu ndi aŵiri ena mosangalala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo msonkhano wonse unapangana kuchita masiku asanu ndi awiri ena, nachita masiku asanu ndi ena ndi chimwemwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo msonkhano wonse unagwirizana zopitiriza chikondwerero kwa masiku ena asanu ndi awiri. Kotero kwa masiku ena asanu ndi awiri anachita chikondwererocho mosangalala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo msonkhano wonse unapangana kucita masiku asanu ndi awiri ena, nacita masiku asanu ndi awiri ena ndi cimwemwe.