2 Chronicles 30:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zimenezi zidakomera mfumu ndi msonkhano wonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo chinthuchi chinayenera m'maso mwa mfumu ndi msonkhano wonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chikonzerochi chinaoneka kuti chinali chabwino kwa mfumu pamodzi ndi anthu onse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo cinthuci cinayenera m'maso mwa mfumu ndi msonkhano wonse.