2 Chronicles 30:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho anthuwo adatsimikiza zoti alengeze ku Israele konse, kuyambira ku Beereseba mpaka ku Dani, kuti anthu abwere kudzachita Paska ya Chauta, Mulungu wa Israele, ku Yerusalemu, pakuti si ambiri ankachita Paskayo monga kudaalembedwera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Motero anakhazikitsa mau kulalikira mwa Israele lonse, kuyambira Beereseba kufikira ku Dani, kuti abwere kuchitira Yehova Mulungu wa Israele Paska ku Yerusalemu; pakuti nthawi yaikulu sanachite monga mudalembedwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anagwirizana zoti alengeze mu Israeli monse kuyambira ku Beeriseba mpaka ku Dani, kuyitana anthu kuti abwere ku Yerusalemu ndi kudzakondwerera Paska wa Yehova, Mulungu wa Israeli. Si ambiri amene ankachita chikondwererochi monga momwe kunalembedwera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Motero anakhazikitsa mau kulalikira mwa Israyeli lonse, kuyambira Beereseba kufikira ku Dani, kuti abwere kucitira Yehova Mulungu wa Israyeli Paskha ku Yerusalemu; pakuti nthawi yaikuru sanacita monga mudalembedwa.
Recommended Reading