2 Chronicles 30:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Musati mukhale ngati makolo anu ndi abale anu amene sadakhulupirire Chauta, Mulungu wa makolo ao, kotero kuti adaŵaononga monga momwe mukuwoneramu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo musamakhala ngati makolo anu ndi abale anu, amene analakwira Yehova Mulungu wa makolo ao, motero kuti anawapereka apasuke, monga mupenya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Musakhale ngati makolo anu ndi abale anu, amene anali osakhulupirika kwa Yehova Mulungu wa makolo awo kotero kuti anawachititsa kuti akhale chinthu chochititsa mantha, monga mukuoneramu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo musamakhala ngati makolo anu ndi abale anu, amene anai akwira Yehova Mulungu wa makolo ao, motero kuti anawapereka apasuke, monga mupenya,